Ezekieli 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Siyani zolakwa zanu zonse zimene munkachita+ ndipo mukhale ndi mtima watsopano* komanso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’
31 Siyani zolakwa zanu zonse zimene munkachita+ ndipo mukhale ndi mtima watsopano* komanso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’