Ezekieli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Unene kuti,‘Kodi mayi anu anali ngati ndani? Anali ngati mkango waukazi pakati pa mikango ina. Ankagona pakati pa mikango yamphamvu,* nʼkumalera ana ake.
2 Unene kuti,‘Kodi mayi anu anali ngati ndani? Anali ngati mkango waukazi pakati pa mikango ina. Ankagona pakati pa mikango yamphamvu,* nʼkumalera ana ake.