Ezekieli 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mkangowo unayambanso kuyendayenda pakati pa mikango ina ndipo unakhala mkango wamphamvu. Unaphunzira kupha nyama ndipo unayamba kudya ngakhale anthu.+
6 Mkangowo unayambanso kuyendayenda pakati pa mikango ina ndipo unakhala mkango wamphamvu. Unaphunzira kupha nyama ndipo unayamba kudya ngakhale anthu.+