Ezekieli 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayi anu anali ngati mtengo wa mpesa*+ umene unadzalidwa mʼmphepete mwa madzi. Mtengowo unabereka zipatso ndipo unali ndi nthambi zambiri chifukwa unali pamadzi ambiri. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:10 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 18-19
10 Mayi anu anali ngati mtengo wa mpesa*+ umene unadzalidwa mʼmphepete mwa madzi. Mtengowo unabereka zipatso ndipo unali ndi nthambi zambiri chifukwa unali pamadzi ambiri.