Ezekieli 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi* za mtengowo zinakhala zolimba, zoyenera kupangira ndodo za olamulira. Mtengowo unakula nʼkutalika kwambiri kuposa mitengo ina,Ndipo unkaonekera patali chifukwa cha kutalika kwake ndiponso kuchuluka kwa masamba ake.
11 Nthambi* za mtengowo zinakhala zolimba, zoyenera kupangira ndodo za olamulira. Mtengowo unakula nʼkutalika kwambiri kuposa mitengo ina,Ndipo unkaonekera patali chifukwa cha kutalika kwake ndiponso kuchuluka kwa masamba ake.