5 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pa tsiku limene ndinasankha Isiraeli,+ ndinalumbiranso kwa ana a Yakobo ndipo ndinawachititsa kuti andidziwe mʼdziko la Iguputo.+ Inde, ndinalumbira kwa iwo nʼkunena kuti, ‘Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’