Ezekieli 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinawapatsanso sabata langa+ kuti likhale chizindikiro pakati pa ine ndi iwowo.+ Ndinachita zimenezi nʼcholinga choti adziwe kuti ine Yehova, ndi amene ndikuwachititsa kuti akhale opatulika.
12 Ndinawapatsanso sabata langa+ kuti likhale chizindikiro pakati pa ine ndi iwowo.+ Ndinachita zimenezi nʼcholinga choti adziwe kuti ine Yehova, ndi amene ndikuwachititsa kuti akhale opatulika.