Ezekieli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinalumbiranso kwa iwo mʼchipululu kuti sindidzawalowetsa mʼdziko limene ndinawapatsa,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi+ komanso lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.
15 Ndinalumbiranso kwa iwo mʼchipululu kuti sindidzawalowetsa mʼdziko limene ndinawapatsa,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi+ komanso lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.