Ezekieli 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinachita zimenezi chifukwa anakana zigamulo zanga, sanatsatire malamulo anga ndipo anadetsa sabata langa popeza anatsimikiza mtima kuti azilambira mafano awo onyansa.+
16 Ndinachita zimenezi chifukwa anakana zigamulo zanga, sanatsatire malamulo anga ndipo anadetsa sabata langa popeza anatsimikiza mtima kuti azilambira mafano awo onyansa.+