Ezekieli 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Muzitsatira malamulo anga ndipo muzisunga zigamulo zanga komanso kuzitsatira.+
19 Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Muzitsatira malamulo anga ndipo muzisunga zigamulo zanga komanso kuzitsatira.+