Ezekieli 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzisunga sabata langa kuti likhale lopatulika+ ndipo lidzakhala chizindikiro pakati pa ine ndi inu, kuti mudziwe kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+
20 Muzisunga sabata langa kuti likhale lopatulika+ ndipo lidzakhala chizindikiro pakati pa ine ndi inu, kuti mudziwe kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’+