Ezekieli 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma sindinatero+ ndipo ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa+ kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.
22 Koma sindinatero+ ndipo ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa+ kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene anaona ndikutulutsa anthu anga pakati pawo.