Ezekieli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ndinalumbira kwa iwo mʼchipululu kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana,+
23 Komanso ndinalumbira kwa iwo mʼchipululu kuti ndidzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana,+