Ezekieli 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso ndinawasiya kuti azitsatira malamulo oipa ndi zigamulo zimene sizikanawathandiza kuti akhale ndi moyo.+
25 Komanso ndinawasiya kuti azitsatira malamulo oipa ndi zigamulo zimene sizikanawathandiza kuti akhale ndi moyo.+