-
Ezekieli 20:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho iwe mwana wa munthu, lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Makolo anu nawonso anandinyoza pondichitira zinthu mosakhulupirika.
-