Ezekieli 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndinawafunsa kuti, ‘Kodi mumakachita chiyani kumalo okwezeka kumene mumapitako? (Malowo akudziwikabe kuti Malo Okwezeka mpaka lero.)’”’+
29 Choncho ndinawafunsa kuti, ‘Kodi mumakachita chiyani kumalo okwezeka kumene mumapitako? (Malowo akudziwikabe kuti Malo Okwezeka mpaka lero.)’”’+