Ezekieli 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Tsopano uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mukudziipitsa ngati mmene makolo anu anachitira potumikira mafano awo onyansa komanso kuwalambira.*+
30 Tsopano uza nyumba ya Isiraeli kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mukudziipitsa ngati mmene makolo anu anachitira potumikira mafano awo onyansa komanso kuwalambira.*+