Ezekieli 20:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ndipo zimene mukuganiza zakuti: “Tiyeni tikhale ngati anthu a mitundu ina. Tikhale ngati mabanja amʼmayiko ena amene amalambira* mitengo ndi miyala,”+ sizichitika.’
32 ‘Ndipo zimene mukuganiza zakuti: “Tiyeni tikhale ngati anthu a mitundu ina. Tikhale ngati mabanja amʼmayiko ena amene amalambira* mitengo ndi miyala,”+ sizichitika.’