Ezekieli 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ‘Ndidzakudutsitsani pansi pa ndodo ya mʼbusa+ ndipo ndidzachititsa kuti musunge pangano.