Ezekieli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lanoledwa kuti liphe anthu ambiri. Lapukutidwa kuti liwale ngati mphezi.’”’” “Kodi sitikuyenera kusangalala?” “‘Kodi lupangalo lidzakana ndodo yachifumu ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse? Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:10 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 19
10 Lanoledwa kuti liphe anthu ambiri. Lapukutidwa kuti liwale ngati mphezi.’”’” “Kodi sitikuyenera kusangalala?” “‘Kodi lupangalo lidzakana ndodo yachifumu ya mwana wanga,+ ngati mmene likukanira mtengo uliwonse?