Ezekieli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Lupangalo ndalipereka kuti lipukutidwe komanso kuti ligwiritsidwe ntchito. Lupanga limeneli lanoledwa komanso kupukutidwa kuti liperekedwe mʼdzanja la munthu wakupha.+
11 Lupangalo ndalipereka kuti lipukutidwe komanso kuti ligwiritsidwe ntchito. Lupanga limeneli lanoledwa komanso kupukutidwa kuti liperekedwe mʼdzanja la munthu wakupha.+