Ezekieli 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe mwana wa munthu, losera ndipo uwombe mʼmanja nʼkunena katatu mawu akuti, ‘Lupanga!’ Limeneli ndi lupanga lopha anthu, lupanga limene lapha anthu ambiri ndipo lawazungulira.+
14 Iwe mwana wa munthu, losera ndipo uwombe mʼmanja nʼkunena katatu mawu akuti, ‘Lupanga!’ Limeneli ndi lupanga lopha anthu, lupanga limene lapha anthu ambiri ndipo lawazungulira.+