Ezekieli 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitima ya anthu idzasungunuka ndi mantha+ ndipo anthu ambiri adzagwa pamageti a mzinda wawo. Ndidzapha anthu ambiri ndi lupanga. Ndithu lupangalo likuwala ngati mphezi ndipo lapukutidwa kuti liphe anthu.
15 Mitima ya anthu idzasungunuka ndi mantha+ ndipo anthu ambiri adzagwa pamageti a mzinda wawo. Ndidzapha anthu ambiri ndi lupanga. Ndithu lupangalo likuwala ngati mphezi ndipo lapukutidwa kuti liphe anthu.