Ezekieli 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso ndidzawomba mʼmanja nʼkupereka chilango ndipo ndikadzatero mkwiyo wanga udzatha.+ Ineyo Yehova ndanena.”
17 Komanso ndidzawomba mʼmanja nʼkupereka chilango ndipo ndikadzatero mkwiyo wanga udzatha.+ Ineyo Yehova ndanena.”