Ezekieli 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa anthu* amene anachita nawo malumbiro, maulawo adzaoneka ngati abodza.+ Koma mfumuyo idzakumbukira zolakwa zawo ndipo idzawagwira.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:23 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 19
23 Kwa anthu* amene anachita nawo malumbiro, maulawo adzaoneka ngati abodza.+ Koma mfumuyo idzakumbukira zolakwa zawo ndipo idzawagwira.+