Ezekieli 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma iwe mtsogoleri wa Isiraeli, amene ndi woipa ndipo wavulazidwa koopsa,+ nthawi yoti ulandire chilango chomaliza yafika. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:25 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 25
25 Koma iwe mtsogoleri wa Isiraeli, amene ndi woipa ndipo wavulazidwa koopsa,+ nthawi yoti ulandire chilango chomaliza yafika.