-
Ezekieli 21:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Iwe mwana wa munthu, losera kuti, ‘Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena zokhudza mbadwa za Amoni ndi mawu awo onyoza.’ Unene kuti, ‘Lupanga! Lupanga lasololedwa kuti liphe anthu. Lapukutidwa kuti liwononge komanso kuti liwale ngati mphezi.
-