Ezekieli 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndidzakukhuthulirani mkwiyo wanga. Ndidzakupemererani ndi moto wa ukali wanga, ndipo ndidzakuperekani mʼmanja mwa anthu ankhanza, akatswiri odziwa kuwononga.+
31 Ndidzakukhuthulirani mkwiyo wanga. Ndidzakupemererani ndi moto wa ukali wanga, ndipo ndidzakuperekani mʼmanja mwa anthu ankhanza, akatswiri odziwa kuwononga.+