Ezekieli 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzakhala ngati nkhuni pamoto.+ Magazi anu adzakhetsedwa mʼdzikolo ndipo simudzakumbukiridwanso, chifukwa ine Yehova ndanena.’”
32 Mudzakhala ngati nkhuni pamoto.+ Magazi anu adzakhetsedwa mʼdzikolo ndipo simudzakumbukiridwanso, chifukwa ine Yehova ndanena.’”