Ezekieli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe mzinda umene uli ndi mlandu wokhetsa magazi,+ umene nthawi yako yoti uweruzidwe ikubwera,+ umenenso umapanga mafano onyansa* kuti udzidetse nawo,+
3 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe mzinda umene uli ndi mlandu wokhetsa magazi,+ umene nthawi yako yoti uweruzidwe ikubwera,+ umenenso umapanga mafano onyansa* kuti udzidetse nawo,+