Ezekieli 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa iwe muli anthu amene salemekeza pogona pa bambo awo*+ ndipo amakakamiza mkazi wodetsedwa amene akusamba kuti agone naye.+
10 Mwa iwe muli anthu amene salemekeza pogona pa bambo awo*+ ndipo amakakamiza mkazi wodetsedwa amene akusamba kuti agone naye.+