-
Ezekieli 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 ‘Ine ndawomba mʼmanja chifukwa chonyansidwa ndi phindu lachinyengo limene wapeza komanso chifukwa cha magazi amene anakhetsedwa pakati pako.
-