Ezekieli 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti nonsenu mwakhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo,+ ine ndikusonkhanitsani pamodzi mu Yerusalemu.
19 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti nonsenu mwakhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo,+ ine ndikusonkhanitsani pamodzi mu Yerusalemu.