-
Ezekieli 22:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mofanana ndi siliva amene amamusungunulira mungʼanjo, inenso ndidzakusungunulirani mumzindawo. Choncho mudzadziwa kuti ine Yehova ndadzakukhuthulirani mkwiyo wanga.’”
-