-
Ezekieli 22:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 “Iwe mwana wa munthu, uza dzikoli kuti, ‘Iwe ndi dziko limene silidzayeretsedwa ndipo mwa iwe simudzagwa mvula pa tsiku limene ndidzakusonyeze mkwiyo wanga.
-