Ezekieli 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala kapena kuima pamalo ogumuka a mpandawo kuti ateteze dzikolo nʼcholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:30 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 20
30 ‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala kapena kuima pamalo ogumuka a mpandawo kuti ateteze dzikolo nʼcholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.