-
Ezekieli 23:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Amunawo anali abwanamkubwa amene ankavala zovala zabuluu ndiponso achiwiri kwa olamulira. Onsewa anali anyamata osiririka, akatswiri okwera mahatchi.
-