Ezekieli 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anapitiriza kuchita uhule ndi amuna onse olemekezeka amʼdziko la Asuri ndipo anadziipitsa+ ndi mafano onyansa* a amuna amene ankawalakalakawo. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:7 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 20-21
7 Iye anapitiriza kuchita uhule ndi amuna onse olemekezeka amʼdziko la Asuri ndipo anadziipitsa+ ndi mafano onyansa* a amuna amene ankawalakalakawo.