Ezekieli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye sanasiye uhule umene ankachita ali ku Iguputo. Aiguputowo ankagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ankasisita pamtima pake ali namwali ndipo ankachita naye zachiwerewere.+
8 Iye sanasiye uhule umene ankachita ali ku Iguputo. Aiguputowo ankagona naye kuyambira ali kamtsikana. Iwo ankasisita pamtima pake ali namwali ndipo ankachita naye zachiwerewere.+