Ezekieli 23:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndatsala pangʼono kukupereka mʼmanja mwa amuna amene ukudana nawo, amuna amene unawasiya chifukwa chonyansidwa nawo.+
28 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndatsala pangʼono kukupereka mʼmanja mwa amuna amene ukudana nawo, amuna amene unawasiya chifukwa chonyansidwa nawo.+