Ezekieli 23:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma amuna olungama adzamupatsa chiweruzo choyenera chimene amapereka kwa munthu wachigololo+ komanso wokhetsa magazi.+ Chifukwa iwowa ndi akazi achigololo ndipo mʼmanja mwawo muli magazi.+
45 Koma amuna olungama adzamupatsa chiweruzo choyenera chimene amapereka kwa munthu wachigololo+ komanso wokhetsa magazi.+ Chifukwa iwowa ndi akazi achigololo ndipo mʼmanja mwawo muli magazi.+