Ezekieli 23:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Adzawabweretsera gulu la asilikali kuti lidzawaukire nʼkuwasandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chinthu choyenera kutengedwa ndi adani.+
46 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Adzawabweretsera gulu la asilikali kuti lidzawaukire nʼkuwasandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chinthu choyenera kutengedwa ndi adani.+