Ezekieli 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Uikemo nthuli za nyama,+ nthuli zabwinozabwino.Uikemo mwendo wamʼmbuyo ndi wakutsogolo. Udzazemo mafupa abwino kwambiri.
4 Uikemo nthuli za nyama,+ nthuli zabwinozabwino.Uikemo mwendo wamʼmbuyo ndi wakutsogolo. Udzazemo mafupa abwino kwambiri.