Ezekieli 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tenga nkhosa yabwino kwambiri+ ndipo usonkhezere nkhuni kuzungulira mphikawo. Uwiritse nthuli za nyamazo limodzi ndi mafupa amene ali mumphikawo.”’
5 Tenga nkhosa yabwino kwambiri+ ndipo usonkhezere nkhuni kuzungulira mphikawo. Uwiritse nthuli za nyamazo limodzi ndi mafupa amene ali mumphikawo.”’