Ezekieli 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi,+ umene uli ngati mphika wadzimbiri, womwe dzimbiri lakelo silikuchoka. Muchotsemo nthulizo imodziimodzi.+ Musachite maere pa nthulizo. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:6 Nsanja ya Olonda,7/1/2007, tsa. 149/15/1988, tsa. 21
6 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Tsoka mzinda wokhetsa magazi,+ umene uli ngati mphika wadzimbiri, womwe dzimbiri lakelo silikuchoka. Muchotsemo nthulizo imodziimodzi.+ Musachite maere pa nthulizo.