Ezekieli 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndathira magazi amene mzindawo wakhetsa pathanthwe lopanda chilichonseKuti asakwiriridwe.+Ndachita zimenezi kuti mkwiyo wanga uyakire mzindawo nʼkuulanga chifukwa cha zochita zake.’
8 Ine ndathira magazi amene mzindawo wakhetsa pathanthwe lopanda chilichonseKuti asakwiriridwe.+Ndachita zimenezi kuti mkwiyo wanga uyakire mzindawo nʼkuulanga chifukwa cha zochita zake.’