Ezekieli 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ikani mphika wakopa* wopanda kanthu pamakala amoto kuti utenthe kwambiriNdipo ufiire chifukwa cha kutentha. Zonyansa zake zisungunukemo+ ndipo dzimbiri lake lipse ndi motowo.
11 Ikani mphika wakopa* wopanda kanthu pamakala amoto kuti utenthe kwambiriNdipo ufiire chifukwa cha kutentha. Zonyansa zake zisungunukemo+ ndipo dzimbiri lake lipse ndi motowo.