Ezekieli 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zikadzatero inu mudzachita zimene ine ndachita. Simudzaphimba ndevu zanu zapamlomo ndipo simudzadya chakudya chimene anthu adzakupatseni.+
22 Zikadzatero inu mudzachita zimene ine ndachita. Simudzaphimba ndevu zanu zapamlomo ndipo simudzadya chakudya chimene anthu adzakupatseni.+