Ezekieli 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mudzavala nduwira zanu ndiponso nsapato zanu. Simudzamva chisoni kapena kulira pagulu. Mʼmalomwake, mudzavutika chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzalira mosatulutsa mawu.
23 Mudzavala nduwira zanu ndiponso nsapato zanu. Simudzamva chisoni kapena kulira pagulu. Mʼmalomwake, mudzavutika chifukwa cha zolakwa zanu+ ndipo mudzalira mosatulutsa mawu.