Ezekieli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Koma iwe mwana wa munthu, pa tsiku limene ndidzawachotsere mpanda wawo wolimba, chinthu chokongola chimene chimawasangalatsa, chinthu chimene amachikonda komanso chapamtima pawo, limodzi ndi ana awo aamuna ndi aakazi,+
25 “Koma iwe mwana wa munthu, pa tsiku limene ndidzawachotsere mpanda wawo wolimba, chinthu chokongola chimene chimawasangalatsa, chinthu chimene amachikonda komanso chapamtima pawo, limodzi ndi ana awo aamuna ndi aakazi,+